Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 23:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Tsopano Yonatani mwana wa Sauli ananyamuka ndi kupita kwa Davide ku Horesi, kuti akalimbikitse+ Davide kudalira Mulungu.+

  • Ezara 6:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kwa masiku 7, iwo anachita mosangalala chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa,+ pakuti Yehova anawachititsa kusangalala. Iye anatembenuzira+ kwa iwo mtima wa mfumu ya Asuri kuti ilimbitse manja awo pa ntchito yomanga nyumba ya Mulungu woona, Mulungu wa Isiraeli.

  • Nehemiya 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Onsewo anali kungofuna kutichititsa mantha, ndipo anali kunena kuti: “Manja awo+ adzalefuka ndipo adzasiya kugwira ntchitoyi, mwakuti siitha.” Inu Mulungu wanga, limbitsani manja anga.+

  • Yesaya 35:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anthu inu limbitsani manja ofooka ndiponso mawondo agwedegwede.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena