Yobu 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aliyense wofuna kugwa, mawu ako anali kumudzutsa,+Ndipo mawondo olobodoka unali kuwachirikiza.+ Luka 22:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma ine ndakupempherera+ iwe kuti chikhulupiriro chako chisathe. Chotero iwenso, ukabwerera, ukalimbikitse+ abale ako.” Aheberi 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho limbitsani manja amene ali lende+ ndi mawondo olobodoka,+
32 Koma ine ndakupempherera+ iwe kuti chikhulupiriro chako chisathe. Chotero iwenso, ukabwerera, ukalimbikitse+ abale ako.”