Yesaya 35:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu inu limbitsani manja ofooka ndiponso mawondo agwedegwede.+ Aheberi 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho limbitsani manja amene ali lende+ ndi mawondo olobodoka,+