Ekisodo 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Muzidzasunga chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa,+ chifukwa pa tsiku limeneli ndidzatulutsa makamu anu m’dziko la Iguputo. Muzidzasunga tsiku limeneli m’mibadwo yanu yonse. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale. Levitiko 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Pa tsiku la 15 m’mwezi umenewu, muzichita chikondwerero cha Yehova cha mikate yopanda chofufumitsa.+ Muzidya mikate yopanda chofufumitsa imeneyi masiku 7.+
17 “‘Muzidzasunga chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa,+ chifukwa pa tsiku limeneli ndidzatulutsa makamu anu m’dziko la Iguputo. Muzidzasunga tsiku limeneli m’mibadwo yanu yonse. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale.
6 “‘Pa tsiku la 15 m’mwezi umenewu, muzichita chikondwerero cha Yehova cha mikate yopanda chofufumitsa.+ Muzidya mikate yopanda chofufumitsa imeneyi masiku 7.+