Numeri 28:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno pa tsiku la 15 la mwezi umenewu pazikhala chikondwerero. Kwa masiku 7 muzidya mikate yopanda chofufumitsa.+ Machitidwe 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ataona kuti zimenezi zasangalatsa Ayuda,+ anamanganso Petulo. (Amenewa anali masiku a mikate yopanda chofufumitsa.)+ 1 Akorinto 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero tiyeni tichite chikondwererochi,+ osati ndi chofufumitsa chakale,+ kapena chofufumitsa+ choimira zoipa ndi uchimo,+ koma ndi mikate yopanda chofufumitsa yoimira kuona mtima ndi choonadi.+
17 Ndiyeno pa tsiku la 15 la mwezi umenewu pazikhala chikondwerero. Kwa masiku 7 muzidya mikate yopanda chofufumitsa.+
3 Ataona kuti zimenezi zasangalatsa Ayuda,+ anamanganso Petulo. (Amenewa anali masiku a mikate yopanda chofufumitsa.)+
8 Chotero tiyeni tichite chikondwererochi,+ osati ndi chofufumitsa chakale,+ kapena chofufumitsa+ choimira zoipa ndi uchimo,+ koma ndi mikate yopanda chofufumitsa yoimira kuona mtima ndi choonadi.+