Yohane 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Popeza Chilamulo chinaperekedwa kudzera mwa Mose,+ kukoma mtima kwakukulu+ komanso choonadi+ zinakhalako kudzera mwa Yesu Khristu. Yohane 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ayeretseni+ ndi choonadi. Mawu+ anu ndiwo choonadi.+
17 Popeza Chilamulo chinaperekedwa kudzera mwa Mose,+ kukoma mtima kwakukulu+ komanso choonadi+ zinakhalako kudzera mwa Yesu Khristu.