Salimo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino,+Ngati siliva woyengedwa nthawi zokwanira 7 mung’anjo ya m’nthaka. Salimo 119:151 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 151 Inu Yehova muli pafupi,+Ndipo malamulo anu onse ndi choonadi.+ Salimo 119:160 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 160 Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha,+Ndipo chigamulo chanu chilichonse cholungama chidzakhalapo mpaka kalekale.+ Yakobo 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti mwa chifuniro+ chake, iye anatibala ife ndi mawu a choonadi.+ Anachita zimenezi kuti tikhale zipatso zoyambirira+ pa zolengedwa zake.
6 Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino,+Ngati siliva woyengedwa nthawi zokwanira 7 mung’anjo ya m’nthaka.
160 Mawu anu onse ndi choonadi chokhachokha,+Ndipo chigamulo chanu chilichonse cholungama chidzakhalapo mpaka kalekale.+
18 Pakuti mwa chifuniro+ chake, iye anatibala ife ndi mawu a choonadi.+ Anachita zimenezi kuti tikhale zipatso zoyambirira+ pa zolengedwa zake.