Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyeno munatsikira paphiri la Sinai+ ndi kulankhula nawo muli kumwamba.+ Munawapatsa zigamulo zowongoka+ ndi malamulo a choonadi,+ mfundo zabwino ndi malangizo abwino.+

  • Salimo 19:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Kuopa+ Yehova n’koyera, ndipo kudzakhalapo kwamuyaya.

      Zigamulo+ za Yehova n’zolondola,+ ndipo pa mbali iliyonse zasonyezadi kuti ndi zolungama.+

  • Salimo 119:142
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 142 Chilungamo chanu ndi chilungamo mpaka kalekale,+

      Ndipo chilamulo chanu ndi choonadi.+

  • Yohane 17:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ayeretseni+ ndi choonadi. Mawu+ anu ndiwo choonadi.+

  • 1 Petulo 1:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Tsopano, popeza mwayeretsa+ miyoyo yanu mwa kukhala omvera choonadi ndipo zotsatira zake n’zakuti mumakonda abale mopanda chinyengo,+ kondanani kwambiri kuchokera mumtima.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena