Ekisodo 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Ndipo izi ndizo zigamulo zoti uwaikire:+ Numeri 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pambuyo pake Yehova anauza Mose kuti: “Munthuyo aphedwe basi!+ Khamu lonselo likam’ponye miyala kunja kwa msasa.”+ Nehemiya 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno munatsikira paphiri la Sinai+ ndi kulankhula nawo muli kumwamba.+ Munawapatsa zigamulo zowongoka+ ndi malamulo a choonadi,+ mfundo zabwino ndi malangizo abwino.+ Salimo 119:137 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 137 Ndinu wolungama inu Yehova,+Ndipo zigamulo zanu ndi zowongoka.+
35 Pambuyo pake Yehova anauza Mose kuti: “Munthuyo aphedwe basi!+ Khamu lonselo likam’ponye miyala kunja kwa msasa.”+
13 Ndiyeno munatsikira paphiri la Sinai+ ndi kulankhula nawo muli kumwamba.+ Munawapatsa zigamulo zowongoka+ ndi malamulo a choonadi,+ mfundo zabwino ndi malangizo abwino.+