Ekisodo 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa tsiku lachitatu akhale okonzeka, chifukwa pa tsiku lachitatulo Yehova adzatsikira paphiri la Sinai pamaso pa anthu onse.+ Deuteronomo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo anati:“Yehova anafika kuchokera ku Sinai,+Anathwanima pa iwo kuchokera ku Seiri.+Anawala kuchokera kudera lamapiri la Parana,+Ndipo anali ndi miyandamiyanda ya oyera ake,+Kudzanja lake lamanja kunali ankhondo ake.+
11 Pa tsiku lachitatu akhale okonzeka, chifukwa pa tsiku lachitatulo Yehova adzatsikira paphiri la Sinai pamaso pa anthu onse.+
2 Ndipo anati:“Yehova anafika kuchokera ku Sinai,+Anathwanima pa iwo kuchokera ku Seiri.+Anawala kuchokera kudera lamapiri la Parana,+Ndipo anali ndi miyandamiyanda ya oyera ake,+Kudzanja lake lamanja kunali ankhondo ake.+