Oweruza 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova, pamene munayenda kuchokera ku Seiri,+Pamene munaguba kuchokera kudera la Edomu,+Dziko linagwedezeka,+ kumwamba kunagwetsa madzi,+Mitambo inagwetsa madzi.
4 Yehova, pamene munayenda kuchokera ku Seiri,+Pamene munaguba kuchokera kudera la Edomu,+Dziko linagwedezeka,+ kumwamba kunagwetsa madzi,+Mitambo inagwetsa madzi.