Deuteronomo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo ndi zigamulo zolungama zofanana ndi chilamulo chonsechi chimene ndikukuikirani pamaso panu lero?+ Deuteronomo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Tsopano amenewa ndiwo malamulo, malangizo ndi zigamulo zimene Yehova Mulungu wanu walamula kuti ndikuphunzitseni,+ kuti muzikazitsatira m’dziko limene mukuwolokerako kukalitenga kukhala lanu. Deuteronomo 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Awa ndi malangizo+ ndi zigamulo+ zimene muyenera kuzitsatira mosamala,+ masiku onse amene mudzakhala m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu adzakulolani kuti mulitenge kukhala lanu.+
8 Ndipo ndi mtundu winanso uti wamphamvu umene uli ndi malangizo ndi zigamulo zolungama zofanana ndi chilamulo chonsechi chimene ndikukuikirani pamaso panu lero?+
6 “Tsopano amenewa ndiwo malamulo, malangizo ndi zigamulo zimene Yehova Mulungu wanu walamula kuti ndikuphunzitseni,+ kuti muzikazitsatira m’dziko limene mukuwolokerako kukalitenga kukhala lanu.
12 “Awa ndi malangizo+ ndi zigamulo+ zimene muyenera kuzitsatira mosamala,+ masiku onse amene mudzakhala m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu adzakulolani kuti mulitenge kukhala lanu.+