10 za tsiku limene munaimirira pamaso pa Yehova Mulungu wanu ku Horebe,+ pamene Yehova anandiuza kuti, ‘Sonkhanitsa anthu kwa ine kuti amve mawu anga,+ naphunzire kundiopa+ masiku onse amene iwo adzakhala ndi moyo padziko, ndi kuti aphunzitsenso ana awo.’+