Ekisodo 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musaope, chifukwa Mulungu woona wabwera+ kuti akuyeseni, ndi kuti mupitirizebe kumuopa kuti musachimwe.”+ Deuteronomo 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zikanakhala bwino kwambiri akanakhala ndi mtima wondiopa+ ndi kusunga malamulo anga+ nthawi zonse, kuti iwo ndi ana awo zinthu ziwayendere bwino mpaka kalekale!*+ 1 Samueli 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma muziopa+ Yehova ndi kum’tumikira ndi mtima wanu wonse m’choonadi.+ Kumbukirani zinthu zazikulu zimene Yehova wakuchitirani.+ Luka 1:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Chifundo chake chakhala pa amene amamuopa ku mibadwomibadwo.+
20 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musaope, chifukwa Mulungu woona wabwera+ kuti akuyeseni, ndi kuti mupitirizebe kumuopa kuti musachimwe.”+
29 Zikanakhala bwino kwambiri akanakhala ndi mtima wondiopa+ ndi kusunga malamulo anga+ nthawi zonse, kuti iwo ndi ana awo zinthu ziwayendere bwino mpaka kalekale!*+
24 Koma muziopa+ Yehova ndi kum’tumikira ndi mtima wanu wonse m’choonadi.+ Kumbukirani zinthu zazikulu zimene Yehova wakuchitirani.+