Ekisodo 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ndimasonyeza kukoma mtima kosatha ku mibadwo masauzande chifukwa cha anthu amene amandikonda ndi kusunga malamulo anga.+ Salimo 103:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma Yehova adzapitiriza kusonyeza kukoma mtima kwake kosatha mpaka kalekale,+Kwa anthu amene amamuopa.+Ndipo adzapitiriza kusonyeza chilungamo chake kwa ana a ana awo.+
6 Koma ndimasonyeza kukoma mtima kosatha ku mibadwo masauzande chifukwa cha anthu amene amandikonda ndi kusunga malamulo anga.+
17 Koma Yehova adzapitiriza kusonyeza kukoma mtima kwake kosatha mpaka kalekale,+Kwa anthu amene amamuopa.+Ndipo adzapitiriza kusonyeza chilungamo chake kwa ana a ana awo.+