Ekisodo 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ndimasonyeza kukoma mtima kosatha ku mibadwo masauzande chifukwa cha anthu amene amandikonda ndi kusunga malamulo anga.+ Salimo 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Adzafika ndi kunena za chilungamo chake,+Adzauza anthu amene adzabadwe kuti iye ndiye wachita zimenezi.+
6 Koma ndimasonyeza kukoma mtima kosatha ku mibadwo masauzande chifukwa cha anthu amene amandikonda ndi kusunga malamulo anga.+
31 Adzafika ndi kunena za chilungamo chake,+Adzauza anthu amene adzabadwe kuti iye ndiye wachita zimenezi.+