Salimo 100:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti Yehova ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapo mpaka kalekale,+Ndipo kukhulupirika kwake kudzakhalapo ku mibadwomibadwo.+ Salimo 118:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 118 Yamikani Yehova anthu inu, pakuti iye ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+ Salimo 136:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 136 Yamikani Yehova anthu inu, pakuti iye ndi wabwino:+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
5 Pakuti Yehova ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapo mpaka kalekale,+Ndipo kukhulupirika kwake kudzakhalapo ku mibadwomibadwo.+
118 Yamikani Yehova anthu inu, pakuti iye ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
136 Yamikani Yehova anthu inu, pakuti iye ndi wabwino:+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+