Salimo 106:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 106 Tamandani Ya, anthu inu!+Yamikani Yehova, chifukwa iye ndi wabwino.+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+ Salimo 107:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 107 Yamikani Yehova anthu inu, pakuti iye ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+ Luka 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yesu anamufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukunditchula kuti wabwino? Palibe wabwino, koma Mulungu yekha.+
106 Tamandani Ya, anthu inu!+Yamikani Yehova, chifukwa iye ndi wabwino.+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
107 Yamikani Yehova anthu inu, pakuti iye ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
19 Yesu anamufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukunditchula kuti wabwino? Palibe wabwino, koma Mulungu yekha.+