Mateyu 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anamuyankha kuti: “N’chifukwa chiyani ukundifunsa chimene chili chabwino? Pali Mmodzi yekha amene ali wabwino.+ Chotero ngati ukufuna kukapeza moyo, uzisunga malamulo nthawi zonse.”+ Maliko 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yesu anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukunditchula kuti wabwino?+ Palibe wabwino, koma Mulungu yekha.+
17 Iye anamuyankha kuti: “N’chifukwa chiyani ukundifunsa chimene chili chabwino? Pali Mmodzi yekha amene ali wabwino.+ Chotero ngati ukufuna kukapeza moyo, uzisunga malamulo nthawi zonse.”+
18 Yesu anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukunditchula kuti wabwino?+ Palibe wabwino, koma Mulungu yekha.+