1 Mbiri 16:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yamikani Yehova anthu inu, chifukwa iye ndi wabwino,+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+ Salimo 118:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 118 Yamikani Yehova anthu inu, pakuti iye ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+ Luka 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yesu anamufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukunditchula kuti wabwino? Palibe wabwino, koma Mulungu yekha.+
34 Yamikani Yehova anthu inu, chifukwa iye ndi wabwino,+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
118 Yamikani Yehova anthu inu, pakuti iye ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
19 Yesu anamufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukunditchula kuti wabwino? Palibe wabwino, koma Mulungu yekha.+