-
Salimo 103:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Koma Yehova adzapitiriza kusonyeza kukoma mtima kwake kosatha mpaka kalekale,+
Kwa anthu amene amamuopa.+
Ndipo adzapitiriza kusonyeza chilungamo chake kwa ana a ana awo.+
-