Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tsopano kwa nthawi yochepa, Yehova Mulungu wathu watikomera mtima+ mwa kutisiyira anthu opulumuka,+ ndiponso mwa kutipatsa malo otetezeka* m’malo ake oyera kuti maso athu awale,+ inu Mulungu wathu, ndi kutitsitsimutsa pang’ono mu ukapolo wathu.+

  • Salimo 77:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Kodi kukoma mtima kwake kosatha wakusiya mpaka muyaya?+

      Kodi malonjezo ake sadzakwaniritsidwa+ ku mibadwomibadwo?

  • Salimo 106:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Zikatero anali kukumbukira pangano limene anachita ndi iwo,+

      Ndipo anali kuwamvera chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwake kosatha.+

  • Malaki 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Ine ndine Yehova, sindinasinthe.+ Inu ndinu ana a Yakobo ndipo simunatheretu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena