Numeri 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+ Aroma 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komabe, sizili ngati kuti mawu a Mulungu analephera.+ Pakuti si onse ochokera kwa Isiraeli amene alidi “Aisiraeli.”+
19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+
6 Komabe, sizili ngati kuti mawu a Mulungu analephera.+ Pakuti si onse ochokera kwa Isiraeli amene alidi “Aisiraeli.”+