Salimo 89:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndalumbira kamodzi kokha pa kuyera kwanga,+Davide sindidzamunamiza.+ Tito 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kumene kwazikidwa pa chiyembekezo cha moyo wosatha,+ chomwe Mulungu amene sanganame,+ analonjeza kalekale.+
2 kumene kwazikidwa pa chiyembekezo cha moyo wosatha,+ chomwe Mulungu amene sanganame,+ analonjeza kalekale.+