Aroma 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa chiyani? Kuti mmene uchimo unalamulira monga mfumu pamodzi ndi imfa,+ momwemonso kukoma mtima kwakukulu+ kulamulire monga mfumu kudzera m’chilungamo. Zimenezi zichitike kuti moyo wosatha+ ubwere kudzera mwa Yesu Khristu Ambuye wathu. Aroma 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa malipiro a uchimo ndi imfa,+ koma mphatso+ imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha+ kudzera mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.+
21 Chifukwa chiyani? Kuti mmene uchimo unalamulira monga mfumu pamodzi ndi imfa,+ momwemonso kukoma mtima kwakukulu+ kulamulire monga mfumu kudzera m’chilungamo. Zimenezi zichitike kuti moyo wosatha+ ubwere kudzera mwa Yesu Khristu Ambuye wathu.
23 Chifukwa malipiro a uchimo ndi imfa,+ koma mphatso+ imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha+ kudzera mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.+