Mateyu 25:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo iwowa adzachoka kupita ku chiwonongeko chotheratu,+ koma olungama ku moyo wosatha.”+ 1 Petulo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anatibereka kuti tikhale ndi cholowa chosawonongeka,+ chosadetsedwa ndiponso chosasuluka. Cholowa chimenechi anasungira inuyo kumwamba,+
4 Anatibereka kuti tikhale ndi cholowa chosawonongeka,+ chosadetsedwa ndiponso chosasuluka. Cholowa chimenechi anasungira inuyo kumwamba,+