Aroma 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa malipiro a uchimo ndi imfa,+ koma mphatso imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha+ kudzera mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:23 Nsanja ya Olonda,4/1/2015, ptsa. 13-148/15/2000, tsa. 132/15/1998, tsa. 24
23 Chifukwa malipiro a uchimo ndi imfa,+ koma mphatso imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha+ kudzera mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.+