1 Timoteyo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komabe, anandichitira chifundo+ kuti Khristu Yesu asonyeze kuleza mtima kwake konse kudzera mwa ine wochimwa kwambiri, kuti chikhale chitsanzo kwa amene adzamukhulupirire+ n’cholinga chakuti adzapeze moyo wosatha.+ 1 Yohane 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ndi nsembe+ yophimba+ machimo athu.+ Osati athu+ okha, komanso a dziko lonse lapansi.+ Yuda 21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 pitirizani kuchita zinthu zimene zingachititse Mulungu kukukondani.+ Chitani zimenezi pamene mukuyembekezera kuti chifundo+ cha Ambuye wathu Yesu Khristu chidzakutsegulireni njira yoti mulandirire moyo wosatha.+
16 Komabe, anandichitira chifundo+ kuti Khristu Yesu asonyeze kuleza mtima kwake konse kudzera mwa ine wochimwa kwambiri, kuti chikhale chitsanzo kwa amene adzamukhulupirire+ n’cholinga chakuti adzapeze moyo wosatha.+
21 pitirizani kuchita zinthu zimene zingachititse Mulungu kukukondani.+ Chitani zimenezi pamene mukuyembekezera kuti chifundo+ cha Ambuye wathu Yesu Khristu chidzakutsegulireni njira yoti mulandirire moyo wosatha.+