Tito 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 kuti titayesedwa olungama+ mwa kukoma mtima kwake kwakukulu,+ tikhale olandira cholowa+ mogwirizana ndi chiyembekezo cha moyo wosatha.+ 1 Yohane 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 (Ife taona ndipo tikuchitira umboni+ ndi kunena kwa inu za moyo wosatha+ umene unachokera kwa Atate ndipo unaonetsedwa kwa ife.)+ 1 Yohane 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndipotu, lonjezo limene iye watipatsa ndi la moyo wosatha.+
7 kuti titayesedwa olungama+ mwa kukoma mtima kwake kwakukulu,+ tikhale olandira cholowa+ mogwirizana ndi chiyembekezo cha moyo wosatha.+
2 (Ife taona ndipo tikuchitira umboni+ ndi kunena kwa inu za moyo wosatha+ umene unachokera kwa Atate ndipo unaonetsedwa kwa ife.)+