Yohane 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+ 1 Yohane 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 (Ife taona ndipo tikuchitira umboni+ ndi kunena kwa inu za moyo wosatha+ umene unachokera kwa Atate ndipo unaonetsedwa kwa ife.)+
3 Pakuti moyo wosatha+ adzaupeza akamaphunzira ndi kudziwa+ za inu, Mulungu yekhayo amene ali woona,+ ndi za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+
2 (Ife taona ndipo tikuchitira umboni+ ndi kunena kwa inu za moyo wosatha+ umene unachokera kwa Atate ndipo unaonetsedwa kwa ife.)+