1 Akorinto 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+ 1 Atesalonika 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti iwo amanena mmene ife tinafikira pakati panu koyamba. Amanenanso mmene inu munatembenukira kwa Mulungu, kusiya mafano+ anu kuti mutumikire Mulungu wamoyo+ ndi woona,+ 1 Yohane 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tikudziwa kuti Mwana wa Mulungu anabwera,+ ndipo anatipatsa nzeru+ kuti timudziwe woonayo.+ Ndipo ife ndife ogwirizana+ ndi woonayo, kudzera mwa Mwana wake Yesu Khristu. Iyeyo ndiye Mulungu woona+ ndiponso wopereka moyo wosatha.+
4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya+ zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano ndi lopanda pake+ m’dziko, ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+
9 Pakuti iwo amanena mmene ife tinafikira pakati panu koyamba. Amanenanso mmene inu munatembenukira kwa Mulungu, kusiya mafano+ anu kuti mutumikire Mulungu wamoyo+ ndi woona,+
20 Tikudziwa kuti Mwana wa Mulungu anabwera,+ ndipo anatipatsa nzeru+ kuti timudziwe woonayo.+ Ndipo ife ndife ogwirizana+ ndi woonayo, kudzera mwa Mwana wake Yesu Khristu. Iyeyo ndiye Mulungu woona+ ndiponso wopereka moyo wosatha.+