Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndiye chifukwa chake, okondedwa anga, thawani+ kupembedza mafano.+

  • 1 Akorinto 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Mukudziwa kuti pamene munali a mitundu ina,+ munali kutsogoleredwa m’njira zosiyanasiyana ku mafano+ osalankhula.+

  • Agalatiya 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ngakhale zili choncho, pamene munali osadziwa Mulungu,+ munali akapolo a zinthu zimene mwachilengedwe si milungu.+

  • 1 Yohane 5:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Inu ana okondedwa, pewani mafano.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena