Deuteronomo 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ukakakhala ndi ana ndi zidzukulu ndipo mwakhala nthawi yaitali m’dzikomo, n’kuchita zinthu zokuwonongetsa+ mwa kupanga chifaniziro,+ chifaniziro cha chinthu chilichonse, n’kuchita choipa pamaso pa Yehova Mulungu wako,+ moti n’kumulakwira, Akolose 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho chititsani ziwalo za thupi+ lanu padziko lapansi kukhala zakufa+ ku dama, zinthu zodetsa, chilakolako cha kugonana,+ chikhumbo choipa, ndi kusirira kwa nsanje,+ kumene ndiko kulambira mafano. 1 Yohane 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu ana okondedwa, pewani mafano.+
25 “Ukakakhala ndi ana ndi zidzukulu ndipo mwakhala nthawi yaitali m’dzikomo, n’kuchita zinthu zokuwonongetsa+ mwa kupanga chifaniziro,+ chifaniziro cha chinthu chilichonse, n’kuchita choipa pamaso pa Yehova Mulungu wako,+ moti n’kumulakwira,
5 Choncho chititsani ziwalo za thupi+ lanu padziko lapansi kukhala zakufa+ ku dama, zinthu zodetsa, chilakolako cha kugonana,+ chikhumbo choipa, ndi kusirira kwa nsanje,+ kumene ndiko kulambira mafano.