1 Akorinto 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Thawani dama.+ Tchimo lililonse limene munthu angachite ndi la kunja kwa thupi lake, koma amene amachita dama amachimwira thupi lake.+ Aefeso 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Dama*+ ndi chonyansa chamtundu uliwonse kapena umbombo+ zisatchulidwe n’komwe pakati panu,+ monga mmene anthu oyera amayenera kuchitira.+ 2 Timoteyo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chotero, thawa zilakolako zaunyamata,+ koma tsatira chilungamo,+ chikhulupiriro, chikondi, ndi mtendere+ limodzi ndi anthu oitana pa Ambuye ndi mtima woyera.+
18 Thawani dama.+ Tchimo lililonse limene munthu angachite ndi la kunja kwa thupi lake, koma amene amachita dama amachimwira thupi lake.+
3 Dama*+ ndi chonyansa chamtundu uliwonse kapena umbombo+ zisatchulidwe n’komwe pakati panu,+ monga mmene anthu oyera amayenera kuchitira.+
22 Chotero, thawa zilakolako zaunyamata,+ koma tsatira chilungamo,+ chikhulupiriro, chikondi, ndi mtendere+ limodzi ndi anthu oitana pa Ambuye ndi mtima woyera.+