1 Akorinto 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Thawani dama.+ Tchimo lililonse limene munthu angachite ndi la kunja kwa thupi lake, koma amene amachita dama amachimwira thupi lake.+ Aefeso 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho samalani kwambiri kuti mmene mukuyendera+ si monga anthu opanda nzeru, koma ngati anzeru.
18 Thawani dama.+ Tchimo lililonse limene munthu angachite ndi la kunja kwa thupi lake, koma amene amachita dama amachimwira thupi lake.+