8 Pakuti kuchita masewera olimbitsa thupi n’kopindulitsa pang’ono, koma kukhala wodzipereka kwa Mulungu+ n’kopindulitsa m’zonse,+ chifukwa kumakhudza lonjezo la moyo uno ndi moyo umene ukubwerawo.+
22 Chotero, thawa zilakolako zaunyamata,+ koma tsatira chilungamo,+ chikhulupiriro, chikondi, ndi mtendere+ limodzi ndi anthu oitana pa Ambuye ndi mtima woyera.+