Mateyu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Taonani! Ndikukutumizani ngati nkhosa pakati pa mimbulu. Choncho muzichita zinthu mochenjera ngati njoka koma moona mtima ngati nkhunda.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:16 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2016, tsa. 29 Nsanja ya Olonda,7/15/1996, tsa. 22
16 Taonani! Ndikukutumizani ngati nkhosa pakati pa mimbulu. Choncho muzichita zinthu mochenjera ngati njoka koma moona mtima ngati nkhunda.+