Mateyu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:16 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2016, tsa. 29 Nsanja ya Olonda,7/15/1996, tsa. 22
16 “Taonani! Ndikukutumizani monga nkhosa pakati pa mimbulu.+ Chotero khalani ochenjera ngati njoka+ koma oona mtima ngati nkhunda.+