Genesis 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano njoka+ inali yochenjera kwambiri+ kuposa nyama zonse zakutchire zimene Yehova Mulungu anapanga.+ Ndipo njokayo inafunsa mkaziyo+ kuti: “Eti n’zoona kuti Mulungu anati musadye zipatso za mtengo uliwonse wa m’mundamu?”+ Aroma 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti anthu onse+ adziwa kuti ndinu omvera. Choncho ndikusangalala chifukwa cha inu. Koma ndikufuna kuti mukhale anzeru+ pa zinthu zabwino, ndi osadziwa+ kanthu pa zinthu zoipa.+
3 Tsopano njoka+ inali yochenjera kwambiri+ kuposa nyama zonse zakutchire zimene Yehova Mulungu anapanga.+ Ndipo njokayo inafunsa mkaziyo+ kuti: “Eti n’zoona kuti Mulungu anati musadye zipatso za mtengo uliwonse wa m’mundamu?”+
19 Pakuti anthu onse+ adziwa kuti ndinu omvera. Choncho ndikusangalala chifukwa cha inu. Koma ndikufuna kuti mukhale anzeru+ pa zinthu zabwino, ndi osadziwa+ kanthu pa zinthu zoipa.+