2 Akorinto 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma nkhawa yanga ndi yakuti mwina, monga mmene njoka inanamizira Hava+ ndi chinyengo chake, maganizo anunso angapotozedwe+ kuti musakhalenso oona mtima ndi oyera ngati mmene muyenera kuchitira kwa Khristu.+ Chivumbulutso 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho chinjokacho+ chinaponyedwa pansi, njoka yakale ija,+ iye wotchedwa Mdyerekezi+ ndi Satana,+ amene akusocheretsa dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu. Iye anaponyedwa kudziko lapansi,+ ndipo angelo akenso anaponyedwa naye limodzi. Chivumbulutso 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako anagwira chinjoka,+ njoka yakale ija,+ amene ndi Mdyerekezi+ ndiponso Satana,+ ndi kumumanga zaka 1,000.
3 Koma nkhawa yanga ndi yakuti mwina, monga mmene njoka inanamizira Hava+ ndi chinyengo chake, maganizo anunso angapotozedwe+ kuti musakhalenso oona mtima ndi oyera ngati mmene muyenera kuchitira kwa Khristu.+
9 Choncho chinjokacho+ chinaponyedwa pansi, njoka yakale ija,+ iye wotchedwa Mdyerekezi+ ndi Satana,+ amene akusocheretsa dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu. Iye anaponyedwa kudziko lapansi,+ ndipo angelo akenso anaponyedwa naye limodzi.
2 Kenako anagwira chinjoka,+ njoka yakale ija,+ amene ndi Mdyerekezi+ ndiponso Satana,+ ndi kumumanga zaka 1,000.