Genesis 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo njokayo inauza mkaziyo kuti: “Kufa simudzafa ayi.+ 1 Timoteyo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso, Adamu sananyengedwe,+ koma mkaziyo ndiye amene ananyengedwa+ ndipo anachimwa.+