Genesis 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano njoka+ inali yochenjera kwambiri+ kuposa nyama zonse zakutchire zimene Yehova Mulungu anapanga.+ Ndipo njokayo inafunsa mkaziyo+ kuti: “Eti n’zoona kuti Mulungu anati musadye zipatso za mtengo uliwonse wa m’mundamu?”+ 2 Akorinto 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma nkhawa yanga ndi yakuti mwina, monga mmene njoka inanamizira Hava+ ndi chinyengo chake, maganizo anunso angapotozedwe+ kuti musakhalenso oona mtima ndi oyera ngati mmene muyenera kuchitira kwa Khristu.+ Chivumbulutso 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma mkaziyo anapatsidwa mapiko awiri+ a chiwombankhanga chachikulu kuti aulukire kuchipululu,+ kumalo ake aja. Kumeneko n’kumene akudyetsedwa+ kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri, ndi hafu ya nthawi,+ kutali ndi njoka ija.+
3 Tsopano njoka+ inali yochenjera kwambiri+ kuposa nyama zonse zakutchire zimene Yehova Mulungu anapanga.+ Ndipo njokayo inafunsa mkaziyo+ kuti: “Eti n’zoona kuti Mulungu anati musadye zipatso za mtengo uliwonse wa m’mundamu?”+
3 Koma nkhawa yanga ndi yakuti mwina, monga mmene njoka inanamizira Hava+ ndi chinyengo chake, maganizo anunso angapotozedwe+ kuti musakhalenso oona mtima ndi oyera ngati mmene muyenera kuchitira kwa Khristu.+
14 Koma mkaziyo anapatsidwa mapiko awiri+ a chiwombankhanga chachikulu kuti aulukire kuchipululu,+ kumalo ake aja. Kumeneko n’kumene akudyetsedwa+ kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri, ndi hafu ya nthawi,+ kutali ndi njoka ija.+