Genesis 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Yehova Mulungu anapanga mkazi kuchokera kunthiti imene anaichotsa kwa mwamunayo. Atatero, anamubweretsa kwa iye.+ Numeri 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Potsirizira pake, Yehova anatsegula pakamwa pa buluyo,+ ndipo buluyo anafunsa Balamu kuti: “Kodi ndakulakwirani chiyani kuti mundikwapule katatu konseka?”+
22 Ndiyeno Yehova Mulungu anapanga mkazi kuchokera kunthiti imene anaichotsa kwa mwamunayo. Atatero, anamubweretsa kwa iye.+
28 Potsirizira pake, Yehova anatsegula pakamwa pa buluyo,+ ndipo buluyo anafunsa Balamu kuti: “Kodi ndakulakwirani chiyani kuti mundikwapule katatu konseka?”+