Chivumbulutso 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ndidzachititsa mboni zanga ziwiri+ kunenera+ kwa masiku 1,260, zitavala ziguduli.”+ Chivumbulutso 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma mkaziyo anathawira kuchipululu,+ kumene Mulungu anamukonzera malo, kuti akadyetsedwe+ masiku 1,260.+
6 Koma mkaziyo anathawira kuchipululu,+ kumene Mulungu anamukonzera malo, kuti akadyetsedwe+ masiku 1,260.+