1 Mafumu 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atayang’ana, anaona kuti kumutu kwake kuli chikho cha madzi ndi mkate wozungulira+ uli pamiyala yotentha. Ndipo Eliya anayamba kudya ndi kumwa, kenako anagonanso. Miyambo 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zachinyengo ndi mawu onama muwaike kutali ndi ine.+ Musandipatse umphawi kapena chuma.+ Ndidye chakudya chimene ndikufunika kudya,+
6 Atayang’ana, anaona kuti kumutu kwake kuli chikho cha madzi ndi mkate wozungulira+ uli pamiyala yotentha. Ndipo Eliya anayamba kudya ndi kumwa, kenako anagonanso.
8 Zachinyengo ndi mawu onama muwaike kutali ndi ine.+ Musandipatse umphawi kapena chuma.+ Ndidye chakudya chimene ndikufunika kudya,+