Miyambo 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Milomo yonama imam’nyansa Yehova,+ koma anthu ochita zinthu mokhulupirika amam’sangalatsa.+ Miyambo 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kupeza chuma pogwiritsa ntchito lilime lonama kuli ngati nkhungu imene imachoka mofulumira.+ Anthu ochita zinthu mwa njira imeneyi akufunafuna imfa.+
6 Kupeza chuma pogwiritsa ntchito lilime lonama kuli ngati nkhungu imene imachoka mofulumira.+ Anthu ochita zinthu mwa njira imeneyi akufunafuna imfa.+