Miyambo 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chuma cha anthu oipa chidzakhala chopanda phindu,+ koma chilungamo n’chimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+ Miyambo 20:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Cholowa chopezedwa mwadyera poyamba,+ tsogolo lake silidzadalitsidwa.+
2 Chuma cha anthu oipa chidzakhala chopanda phindu,+ koma chilungamo n’chimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+