Miyambo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zinthu zamtengo wapatali zidzakhala zopanda phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+ koma chilungamo n’chimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+ Miyambo 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 M’njira yachilungamo muli moyo,+ ndipo ulendo wa m’njira imeneyi suthera ku imfa.+ Danieli 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chotero inu mfumu, chonde mverani malangizo anga+ ndipo chotsani machimo anu pochita zolungama.+ Muchotsenso zolakwa zanu pochitira chifundo osauka.+ Mukatero, mwina zinthu zidzapitiriza kukuyenderani bwino kwa nthawi yaitali.’”+
4 Zinthu zamtengo wapatali zidzakhala zopanda phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+ koma chilungamo n’chimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+
27 Chotero inu mfumu, chonde mverani malangizo anga+ ndipo chotsani machimo anu pochita zolungama.+ Muchotsenso zolakwa zanu pochitira chifundo osauka.+ Mukatero, mwina zinthu zidzapitiriza kukuyenderani bwino kwa nthawi yaitali.’”+