Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 16:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Cholakwa chimaphimbika ndi kukoma mtima kosatha ndiponso choonadi,+ ndipo chifukwa choopa Yehova munthu amapatuka pa choipa.+

  • Miyambo 28:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+ koma woulula n’kuwasiya adzachitiridwa chifundo.+

  • Yesaya 55:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Munthu woipa asiye njira yake+ ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.+ Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+ Abwerere kwa Mulungu wathu, pakuti amakhululuka ndi mtima wonse.+

  • Ezekieli 18:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “‘Munthu woipa akabwerera, kusiya machimo ake onse amene anali kuchita+ ndipo akasunga malamulo anga onse n’kuchita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo,+ adzakhalabe ndi moyo. Sadzafa ayi.+

  • Mateyu 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndiyetu mubale zipatso zosonyeza kulapa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena