2 Samueli 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Davide anauza+ Natani kuti: “Ndachimwira Yehova.”+ Ndiyeno Natani anauza Davide kuti: “Yehova wakukhululukira tchimo lako+ ndipo suufa.+ 2 Mbiri 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye atasautsika mumtima mwake chifukwa cha zimenezi,+ anakhazikitsa pansi mtima wa Yehova Mulungu wake+ ndipo anadzichepetsa+ kwambiri pamaso pa Mulungu wa makolo ake. Salimo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu, ndipo sindinabise cholakwa changa.+Ndinati: “Ndidzaulula kwa Yehova machimo anga.”+Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ [Seʹlah.] Salimo 51:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha.+Malinga ndi kuchuluka kwa chifundo chanu, fafanizani zolakwa zanga.+
13 Pamenepo Davide anauza+ Natani kuti: “Ndachimwira Yehova.”+ Ndiyeno Natani anauza Davide kuti: “Yehova wakukhululukira tchimo lako+ ndipo suufa.+
12 Iye atasautsika mumtima mwake chifukwa cha zimenezi,+ anakhazikitsa pansi mtima wa Yehova Mulungu wake+ ndipo anadzichepetsa+ kwambiri pamaso pa Mulungu wa makolo ake.
5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu, ndipo sindinabise cholakwa changa.+Ndinati: “Ndidzaulula kwa Yehova machimo anga.”+Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ [Seʹlah.]
51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, malinga ndi kukoma mtima kwanu kosatha.+Malinga ndi kuchuluka kwa chifundo chanu, fafanizani zolakwa zanga.+